Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+
6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+