Deuteronomo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amene amadana naye adzawabwezera powawononga.+ Iye sadzazengereza kupereka chilango kwa anthu amene amadana naye koma adzawabwezera powawononga.
10 Koma anthu amene amadana naye adzawabwezera powawononga.+ Iye sadzazengereza kupereka chilango kwa anthu amene amadana naye koma adzawabwezera powawononga.