19 Muzikumbukira ziweruzo zamphamvu zimene maso anu anaona, zizindikiro, zodabwitsa,+ dzanja lamphamvu ndiponso mkono wotambasula umene Yehova Mulungu wanu anagwiritsa ntchito pokutulutsani mʼdzikolo.+ Izi ndi zimene Yehova Mulungu wanu adzachite ndi anthu a mitundu yonse amene mukuwaopa.+