Deuteronomo 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, Mulungu wamphamvu komanso wochititsa mantha,+ ali pakati panu.+
21 Musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, Mulungu wamphamvu komanso wochititsa mantha,+ ali pakati panu.+