Deuteronomo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.
22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.