Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 amene anakuyendetsani mʼchipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni, zinkhanira ndiponso nthaka youma yopanda madzi. Iye anachititsa kuti madzi atuluke pamwala wolimba,+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:15 Nsanja ya Olonda,5/1/1992, tsa. 24
15 amene anakuyendetsani mʼchipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni, zinkhanira ndiponso nthaka youma yopanda madzi. Iye anachititsa kuti madzi atuluke pamwala wolimba,+