Deuteronomo 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzatheratu mofanana ndi mitundu imene Yehova akuiwononga pamaso panu, chifukwa simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.”+
20 Mudzatheratu mofanana ndi mitundu imene Yehova akuiwononga pamaso panu, chifukwa simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.”+