Deuteronomo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa mʼdziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba,*+
9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa mʼdziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba,*+