Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Nsanja ya Olonda,12/1/1996, tsa. 30
7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+