Deuteronomo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale ku Horebe, inu munakwiyitsa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri ndipo ankafuna kukuwonongani.+
8 Ngakhale ku Horebe, inu munakwiyitsa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri ndipo ankafuna kukuwonongani.+