Deuteronomo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.
9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.