Deuteronomo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nditayangʼana, ndinaona kuti mwachimwira Yehova Mulungu wanu. Munali mutadzipangira mwana wa ngʼombe wachitsulo.* Munali mutapatuka mofulumira panjira imene Yehova anakulamulani kuti muziyendamo.+
16 Nditayangʼana, ndinaona kuti mwachimwira Yehova Mulungu wanu. Munali mutadzipangira mwana wa ngʼombe wachitsulo.* Munali mutapatuka mofulumira panjira imene Yehova anakulamulani kuti muziyendamo.+