Deuteronomo 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anakwiyira kwambiri Aroni, moti ankafuna kumuwononga,+ koma ine ndinapembedzera Mulungu pa nthawi imeneyonso kuti asawononge Aroni.
20 Yehova anakwiyira kwambiri Aroni, moti ankafuna kumuwononga,+ koma ine ndinapembedzera Mulungu pa nthawi imeneyonso kuti asawononge Aroni.