Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuwonjezera pamenepo, munaputanso mkwiyo wa Yehova ku Tabera,+ ku Masa+ ndi ku Kibiroti-hatava.+