Deuteronomo 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukapanda kutero, anthu amʼdziko limene munatitulutsamo adzanena kuti: “Yehova sanathe kuwalowetsa mʼdziko limene anawalonjeza komanso chifukwa chakuti ankadana nawo, anawatulutsa kuti akawaphe mʼchipululu.”+
28 Mukapanda kutero, anthu amʼdziko limene munatitulutsamo adzanena kuti: “Yehova sanathe kuwalowetsa mʼdziko limene anawalonjeza komanso chifukwa chakuti ankadana nawo, anawatulutsa kuti akawaphe mʼchipululu.”+