-
Deuteronomo 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Pamiyalayo ndidzalembapo mawu amene anali pamiyala yoyamba ija, imene unaiswa, ndipo udzaiike mʼlikasalo.’