Deuteronomo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo mʼlikasa limene ndinapanga. Mpaka pano miyalayo idakali momwemo, mogwirizana ndi zimene Yehova anandilamula. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 31
5 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo mʼlikasa limene ndinapanga. Mpaka pano miyalayo idakali momwemo, mogwirizana ndi zimene Yehova anandilamula.