Deuteronomo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Muzikonda Yehova Mulungu wanu+ ndipo nthawi zonse muzichita zofuna zake, kutsatira malangizo ake, zigamulo zake komanso malamulo ake.
11 “Muzikonda Yehova Mulungu wanu+ ndipo nthawi zonse muzichita zofuna zake, kutsatira malangizo ake, zigamulo zake komanso malamulo ake.