Deuteronomo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo mukudziwa kuti lero ndikulankhula ndi inu, osati ndi ana anu amene sakudziwa komanso sanaone chilango cha Yehova Mulungu wanu,+ ukulu wake,+ dzanja lake lamphamvu+ komanso mkono wake wotambasula.
2 Inuyo mukudziwa kuti lero ndikulankhula ndi inu, osati ndi ana anu amene sakudziwa komanso sanaone chilango cha Yehova Mulungu wanu,+ ukulu wake,+ dzanja lake lamphamvu+ komanso mkono wake wotambasula.