Deuteronomo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sanaonenso zimene Mulungu anachitira gulu la asilikali a ku Aiguputo, mahatchi a Farao ndi magaleta ake ankhondo, amene anamira mʼmadzi a mʼNyanja Yofiira pamene ankakuthamangitsani, ndipo Yehova anawawononga nʼkutheratu.+
4 Sanaonenso zimene Mulungu anachitira gulu la asilikali a ku Aiguputo, mahatchi a Farao ndi magaleta ake ankhondo, amene anamira mʼmadzi a mʼNyanja Yofiira pamene ankakuthamangitsani, ndipo Yehova anawawononga nʼkutheratu.+