-
Deuteronomo 11:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Muzisunga malamulo onse amene ndikukupatsani lero, kuti mukhale amphamvu nʼkulowa mʼdziko limene mukuwolokerako kuti mukalitenge kukhala lanu,
-