-
Deuteronomo 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Limeneli ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kumayambiriro kwa chaka mpaka kumapeto.
-