Deuteronomo 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke nʼkupatuka ndi kuyamba kulambira milungu ina nʼkumaiweramira.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2019, ptsa. 3-4
16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke nʼkupatuka ndi kuyamba kulambira milungu ina nʼkumaiweramira.+