Deuteronomo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo iye adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ komanso nthaka sidzapereka zokolola zake. Zikadzatero mudzatha mofulumira mʼdziko labwino limene Yehova akukupatsani.+
17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo iye adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ komanso nthaka sidzapereka zokolola zake. Zikadzatero mudzatha mofulumira mʼdziko labwino limene Yehova akukupatsani.+