Deuteronomo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibe munthu amene adzalimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzayendemo kugwidwa ndi mantha aakulu ndipo adzakuopani,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.
25 Palibe munthu amene adzalimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzayendemo kugwidwa ndi mantha aakulu ndipo adzakuopani,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.