Deuteronomo 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 mudzalandira dalitsoli mukadzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupatsani lero,+