Deuteronomo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 ndipo mudzalandira temberero limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ nʼkupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo nʼkuyamba kutsatira milungu imene simukuidziwa.
28 ndipo mudzalandira temberero limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ nʼkupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo nʼkuyamba kutsatira milungu imene simukuidziwa.