Deuteronomo 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu, mukatchule dalitsoli paphiri la Gerizimu ndipo temberero mukalitchulire* paphiri la Ebala.+
29 Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu, mukatchule dalitsoli paphiri la Gerizimu ndipo temberero mukalitchulire* paphiri la Ebala.+