Deuteronomo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pajatu mapiri amenewa ali kutsidya lina la mtsinje wa Yorodano chakumadzulo,* mʼdziko la Akanani amene akukhala ku Araba, moyangʼanizana ndi Giligala, pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More.+
30 Pajatu mapiri amenewa ali kutsidya lina la mtsinje wa Yorodano chakumadzulo,* mʼdziko la Akanani amene akukhala ku Araba, moyangʼanizana ndi Giligala, pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More.+