Deuteronomo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukawonongeretu malo onse amene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo,+ kaya ndi pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.
2 Mukawonongeretu malo onse amene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo,+ kaya ndi pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.