Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+
3 Mukagwetse maguwa awo ansembe nʼkuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mukawotche mizati yawo yopatulika* nʼkudula zifaniziro zogoba za milungu yawo,+ ndipo mukachotseretu mayina awo pamalo amenewo.+