Deuteronomo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.
7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.