Deuteronomo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukawoloka Yorodano+ nʼkukakhala mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu, adzakutetezani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhala otetezeka.+
10 Mukawoloka Yorodano+ nʼkukakhala mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu, adzakutetezani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhala otetezeka.+