Deuteronomo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mudzasangalala pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ inuyo ndi ana anu aamuna, ana anu aakazi, akapolo anu aamuna, akapolo anu aakazi ndi Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,* chifukwa iye sanapatsidwe gawo kapena cholowa mofanana ndi inu.+
12 Mudzasangalala pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ inuyo ndi ana anu aamuna, ana anu aakazi, akapolo anu aamuna, akapolo anu aakazi ndi Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,* chifukwa iye sanapatsidwe gawo kapena cholowa mofanana ndi inu.+