Deuteronomo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mʼdera limodzi mwa madera a mafuko anu, ndipo pamalo amenewo muzidzachita chilichonse chimene ndakulamulani.+
14 Muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mʼdera limodzi mwa madera a mafuko anu, ndipo pamalo amenewo muzidzachita chilichonse chimene ndakulamulani.+