Deuteronomo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mungathe kuidya ngati mmene mungadyere insa ndi mbawala.+ Munthu wodetsedwa komanso munthu wosadetsedwa angathe kudya nyamayo.
22 Mungathe kuidya ngati mmene mungadyere insa ndi mbawala.+ Munthu wodetsedwa komanso munthu wosadetsedwa angathe kudya nyamayo.