Deuteronomo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mungokhala otsimikiza mtima kuti musadye magazi,+ chifukwa magazi ndi moyo,+ ndipo musamadye nyama limodzi ndi moyo wake. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:23 Nsanja ya Olonda,6/15/1991, tsa. 31
23 Koma mungokhala otsimikiza mtima kuti musadye magazi,+ chifukwa magazi ndi moyo,+ ndipo musamadye nyama limodzi ndi moyo wake.