-
Deuteronomo 13:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 “Pakati panu pakapezeka mneneri kapena wolosera za mʼtsogolo pogwiritsa ntchito maloto nʼkukupatsani chizindikiro kapena kulosera china chake,
-