Deuteronomo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 musamvere mawu a mneneriyo kapena woloserayo,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukuyesani+ kuti adziwe ngati mumakonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.+
3 musamvere mawu a mneneriyo kapena woloserayo,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukuyesani+ kuti adziwe ngati mumakonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.+