Deuteronomo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 muzifufuza mosamala kwambiri komanso muzifunsa ena za nkhaniyo.+ Ndiye zikatsimikizirika kuti ndi zoonadi kuti chinthu chonyansachi chachitika pakati panu,
14 muzifufuza mosamala kwambiri komanso muzifunsa ena za nkhaniyo.+ Ndiye zikatsimikizirika kuti ndi zoonadi kuti chinthu chonyansachi chachitika pakati panu,