17 Dzanja lanu lisatenge chinthu chilichonse choyenera kuwonongedwa,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani ndiponso kuti akuchitireni chifundo, kukumverani chisoni ndi kukuchulukitsani, mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu.+