Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2004, tsa. 27
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+