Deuteronomo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa zinthu zonse zokhala mʼmadzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chimene chili ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+
9 Pa zinthu zonse zokhala mʼmadzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chimene chili ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+