-
Deuteronomo 14:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma musamadye chilichonse chimene chilibe zipsepse ndi mamba. Chimenecho nʼchodetsedwa kwa inu.