Deuteronomo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumapeto kwa zaka zitatu zilizonse muzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zanu zonse mʼchaka chachitatucho, ndipo muzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.+
28 Kumapeto kwa zaka zitatu zilizonse muzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zanu zonse mʼchaka chachitatucho, ndipo muzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.+