Deuteronomo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsani ndithu+ mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.
4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsani ndithu+ mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.