Deuteronomo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma muzithandiza mʼbale wanuyo mowolowa manja,+ ndipo mulimonse mmene zingakhalire, muzimukongoza* chilichonse chimene akufuna kapena chimene akusowa. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:8 Nsanja ya Olonda,9/15/2010, tsa. 8
8 Koma muzithandiza mʼbale wanuyo mowolowa manja,+ ndipo mulimonse mmene zingakhalire, muzimukongoza* chilichonse chimene akufuna kapena chimene akusowa.