Deuteronomo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muzimupatsa mowolowa manja zimene akufunazo,+ ndipo musamamupatse* zinthuzo monyinyirika. Mukamachita zimenezi, Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita ndi ntchito zanu zonse.+
10 Muzimupatsa mowolowa manja zimene akufunazo,+ ndipo musamamupatse* zinthuzo monyinyirika. Mukamachita zimenezi, Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita ndi ntchito zanu zonse.+