-
Deuteronomo 15:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Muzikumbukira kuti munali akapolo mʼdziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wanu anakuwombolani. Nʼchifukwa chake lero ndikukulamulani kuti muzichita zinthu zimenezi.
-