-
Deuteronomo 15:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Musamaone kuti sipanachitike chilungamo ngati kapolo wanu mwamumasula iye nʼkuchoka, chifukwa ntchito imene wakugwirirani kwa zaka 6 ndi yochuluka kuwirikiza kawiri kuposa ya munthu waganyu, ndipo Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse.
-